MASSA ladandaula ndi FAM pomuyitana Gabadinho Mhango ku camp ya Flames kukhonzekela Zimbabwe – Zampirampira.com – Football, Netball, Basketball, Hockey,Tennis and sports in Malawi

MASSA ladandaula ndi FAM pomuyitana Gabadinho Mhango ku camp ya Flames kukhonzekela Zimbabwe

Share Button

Bungwe la Malawi Schools Sports Association (MASSA) ladandaula ndizimene anapanga a FAM pomuyitana Gabadinho Mhango ku camp ya Flames komanso pomulowetsa game ya Zimbabwe.

”The game was a friendly one. Gaba is a Form 2 kid. He is suppossed to be in school studying and not playing football. Why FAM called him into camp is just inconsiderate to his future. A FAM akupangilanji zimenezi. Kodi akufuna kuti akanike kulemba mayeso ngati chaka chathanso?” adandaula a MASSA

”kodi nawo a MASSA angothi mfwii mfwiii panopa pamene Gaba yo adasewera kale masewero wo bwanji? Samanena atamutenga ku camp ko bwanji?” a John Kaputa a FAM adabwa motero

Share Button

2 Comments

Leave a Comment

(required)

(required)