Timu ya Be Forword Wanderers sikuchita bwino mupikisano wa TNM Super League zomwe zapagwitsa Mlembi Mike Butao adzuzule aphuzitsi mu timuyi.
A Butao ayakhula izi pomwe timu yawo ya ludza ndi Nyasa Big Bullets Sabata yathayi.
“ Ndikuwona ngati vuto anziphuzitsi,”atero a Butao.
Komabe, wa chiwiri wa pa mpando wa timuyi , Gift Mkandawire wati sibwino kumangodandaula za kugonja ndi timu ya Bullets koma tsopano ayenela kuyang’ana kutsogolo monga kupanga zoti atenge chikho cha Fisd challenge.
Leave a Comment